-
Ekisodo 8:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Mawa ulawirire mʼmamawa kwambiri kukakumana ndi Farao akamadzapita kumtsinje, ndipo ukamuuze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Lola anthu anga apite kuti akanditumikire.
-