21 Koma ngati sulola kuti anthu anga apite, nditumiza ntchentche zoluma kwa iweyo, atumiki ako, anthu ako ndi mʼnyumba zanu. Ndipo nyumba za mu Iguputo zidzangodzaziratu ndi ntchentche zimenezi komanso pena paliponse pamene pali anthu moti adzasowa poponda.