Ekisodo 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiyeno Farao anati: “Ineyo ndikulolani kuti mupite, ndipo mukaperekadi nsembe kwa Yehova Mulungu wanu mʼchipululu, koma musapite kutali kwambiri. Ndichonderereni kwa Mulungu wanu.”+
28 Ndiyeno Farao anati: “Ineyo ndikulolani kuti mupite, ndipo mukaperekadi nsembe kwa Yehova Mulungu wanu mʼchipululu, koma musapite kutali kwambiri. Ndichonderereni kwa Mulungu wanu.”+