Ekisodo 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kenako Mose anati: “Ndikachoka pano, ndikupita kukakuchondererani kwa Yehova ndipo mawa ntchentchezi zichoka pa inu Farao, atumiki anu ndi anthu anu. Koma inu Farao musatipusitsenso posalola anthu kupita kuti akapereke nsembe kwa Yehova.”+
29 Kenako Mose anati: “Ndikachoka pano, ndikupita kukakuchondererani kwa Yehova ndipo mawa ntchentchezi zichoka pa inu Farao, atumiki anu ndi anthu anu. Koma inu Farao musatipusitsenso posalola anthu kupita kuti akapereke nsembe kwa Yehova.”+