-
Ekisodo 8:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Choncho Yehova anachita mogwirizana ndi zimene Mose anapempha, ndipo ntchentchezo zinachoka kwa Farao, atumiki ake ndi anthu ake. Sipanatsale ntchentche ngakhale imodzi.
-