Ekisodo 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Choncho Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa Farao, ukamuuze kuti, ‘Yehova Mulungu wa Aheberi wanena kuti: “Lola anthu anga apite kuti akanditumikire.+
9 Choncho Yehova anauza Mose kuti: “Pita kwa Farao, ukamuuze kuti, ‘Yehova Mulungu wa Aheberi wanena kuti: “Lola anthu anga apite kuti akanditumikire.+