Ekisodo 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndiye Farao atafufuza anapeza kuti palibe chiweto ngakhale chimodzi cha Aisiraeli chimene chinafa. Ngakhale zinali choncho, Farao anapitiriza kuumitsa mtima wake ndipo sanalole kuti Aisiraeli apite.+
7 Ndiye Farao atafufuza anapeza kuti palibe chiweto ngakhale chimodzi cha Aisiraeli chimene chinafa. Ngakhale zinali choncho, Farao anapitiriza kuumitsa mtima wake ndipo sanalole kuti Aisiraeli apite.+