-
Ekisodo 9:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Ndipo lidzachuluka nʼkugwa ngati fumbi padziko lonse la Iguputo. Likatero lidzayambitsa zithupsa pa anthu ndi nyama zomwe, mʼdziko lonse la Iguputo.”
-