-
Ekisodo 9:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Kenako Yehova anauza Mose kuti: “Mawa ulawirire mʼmamawa kwambiri kukaonana ndi Farao, ndipo ukamuuze kuti: ‘Yehova Mulungu wa Aheberi wanena kuti: “Lola anthu anga apite kuti akanditumikire.
-