-
Ekisodo 9:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Taona, mawa pa nthawi ngati ino ndigwetsa mvula yamphamvu kwambiri yamatalala, matalala amene sanayambe agwapo mu Iguputo mʼmbiri yonse ya dzikoli mpaka lero.
-