-
Ekisodo 9:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Choncho tumiza atumiki ako kuti asonkhanitse ziweto zako zonse ndi zinthu zako zonse zimene zili kunja nʼkuzilowetsa mʼmalo otetezeka. Munthu aliyense komanso nyama iliyonse imene idzapezeke kunja osati mʼnyumba, idzafa chifukwa matalalawo adzawagwera.”’”
-