Ekisodo 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipo kunagwa matalala komanso moto unkangʼanima. Kunagwa matalala amphamvu kwambiri amene sanaonekepo nʼkale lonse mʼdziko lonse la Iguputo.+
24 Ndipo kunagwa matalala komanso moto unkangʼanima. Kunagwa matalala amphamvu kwambiri amene sanaonekepo nʼkale lonse mʼdziko lonse la Iguputo.+