Ekisodo 9:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Matalalawo anawononga china chilichonse mʼdziko lonse la Iguputo. Anapha anthu komanso nyama ndipo anawononga zomera zonse zamʼmunda. Anagwetsanso mitengo yonse yamʼdzikolo.+
25 Matalalawo anawononga china chilichonse mʼdziko lonse la Iguputo. Anapha anthu komanso nyama ndipo anawononga zomera zonse zamʼmunda. Anagwetsanso mitengo yonse yamʼdzikolo.+