Ekisodo 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pa nthawi imeneyo mbewu za fulakesi* ndi balere zinawonongeka, chifukwa balere anali atakhwima ndipo fulakesi anali atachita maluwa.
31 Pa nthawi imeneyo mbewu za fulakesi* ndi balere zinawonongeka, chifukwa balere anali atakhwima ndipo fulakesi anali atachita maluwa.