Ekisodo 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Anthu sankatha kuonana ndipo palibe amene anachoka pamalo amene anali kwa masiku atatu. Koma kumene Aisiraeli ankakhala kunkawala.+
23 Anthu sankatha kuonana ndipo palibe amene anachoka pamalo amene anali kwa masiku atatu. Koma kumene Aisiraeli ankakhala kunkawala.+