-
Ekisodo 12:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Koma ngati banja lili lalingʼono moti silingamalize kudya nkhosa yonseyo, banjalo lidzaitane banja lina loyandikana nalo kuti adzadyere limodzi mʼnyumba mwawo, mogwirizana ndi chiwerengero cha anthu. Muziganizira mmene munthu aliyense amadyera kuti mudziwe kuchuluka kwa nyama imene ikufunika.
-