Ekisodo 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kudya kwake mudzadye chonchi, mudzakhale mutamanga lamba mʼchiuno mwanu, mutavala nsapato ndiponso mutatenga ndodo mʼdzanja lanu. Muzidzadya mofulumira. Ameneyu ndi Pasika* wa Yehova.
11 Kudya kwake mudzadye chonchi, mudzakhale mutamanga lamba mʼchiuno mwanu, mutavala nsapato ndiponso mutatenga ndodo mʼdzanja lanu. Muzidzadya mofulumira. Ameneyu ndi Pasika* wa Yehova.