Ekisodo 12:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Muzidzachita Chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa,+ chifukwa pa tsiku limeneli ndidzatulutsa makamu anu mʼdziko la Iguputo. Muzidzasunga tsiku limeneli mʼmibadwo yanu yonse. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale.
17 Muzidzachita Chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa,+ chifukwa pa tsiku limeneli ndidzatulutsa makamu anu mʼdziko la Iguputo. Muzidzasunga tsiku limeneli mʼmibadwo yanu yonse. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale.