Ekisodo 12:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Choncho Aisiraeli ananyamula ufa wokanda wopanda zofufumitsa. Anaunyamulira mʼzokandiramo ufa* pamapewa awo atazikulunga mʼnsalu zawo.
34 Choncho Aisiraeli ananyamula ufa wokanda wopanda zofufumitsa. Anaunyamulira mʼzokandiramo ufa* pamapewa awo atazikulunga mʼnsalu zawo.