Ekisodo 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Muzidzadya mikate yopanda zofufumitsa kwa masiku 7.+ Musamadzapezeke ndi chilichonse chokhala ndi zofufumitsa.+ Ufa wokanda wokhala ndi zofufumitsa usamadzapezeke pena paliponse mʼdziko lanu.
7 Muzidzadya mikate yopanda zofufumitsa kwa masiku 7.+ Musamadzapezeke ndi chilichonse chokhala ndi zofufumitsa.+ Ufa wokanda wokhala ndi zofufumitsa usamadzapezeke pena paliponse mʼdziko lanu.