Ekisodo 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mwambowu ukhale ngati chizindikiro cholembedwa padzanja lanu ndi pamphumi panu.*+ Uzikukumbutsani kuti muzilankhula za chilamulo cha Yehova. Uzikukumbutsaninso kuti Yehova ndi amene anakutulutsani mʼdziko la Iguputo ndi dzanja lake lamphamvu.
9 Mwambowu ukhale ngati chizindikiro cholembedwa padzanja lanu ndi pamphumi panu.*+ Uzikukumbutsani kuti muzilankhula za chilamulo cha Yehova. Uzikukumbutsaninso kuti Yehova ndi amene anakutulutsani mʼdziko la Iguputo ndi dzanja lake lamphamvu.