Ekisodo 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 muzidzapereka kwa Yehova mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa,* wa munthu komanso wa chiweto. Chachimuna chilichonse ndi cha Yehova.+
12 muzidzapereka kwa Yehova mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa,* wa munthu komanso wa chiweto. Chachimuna chilichonse ndi cha Yehova.+