Ekisodo 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mwambowu ukhale ngati chizindikiro cholembedwa padzanja lanu komanso pamphumi panu,*+ chifukwa Yehova anatitulutsa mu Iguputo ndi dzanja lake lamphamvu.”
16 Mwambowu ukhale ngati chizindikiro cholembedwa padzanja lanu komanso pamphumi panu,*+ chifukwa Yehova anatitulutsa mu Iguputo ndi dzanja lake lamphamvu.”