Ekisodo 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chipilala cha mtambo sichinkachoka patsogolo pa anthuwo masana, komanso chipilala cha moto sichinkachoka patsogolo pawo usiku.+
22 Chipilala cha mtambo sichinkachoka patsogolo pa anthuwo masana, komanso chipilala cha moto sichinkachoka patsogolo pawo usiku.+