Ekisodo 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma anthuwo anali ndi ludzu kwambiri ndipo anapitiriza kungʼungʼudza motsutsana ndi Mose+ kuti: “Nʼchifukwa chiyani unatitulutsa ku Iguputo kuti udzatiphe ndi ludzu limodzi ndi ana athu ndi ziweto zathu?”
3 Koma anthuwo anali ndi ludzu kwambiri ndipo anapitiriza kungʼungʼudza motsutsana ndi Mose+ kuti: “Nʼchifukwa chiyani unatitulutsa ku Iguputo kuti udzatiphe ndi ludzu limodzi ndi ana athu ndi ziweto zathu?”