Ekisodo 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tamvera! Ine ndidzatsogola nʼkukaima pathanthwe ku Horebe. Kumeneko ukamenye thanthwelo ndipo padzatuluka madzi amene anthu adzamwe.”+ Mose anachitadi zomwezo pamaso pa akulu a Isiraeli. Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:6 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),7/2018, ptsa. 13-14
6 Tamvera! Ine ndidzatsogola nʼkukaima pathanthwe ku Horebe. Kumeneko ukamenye thanthwelo ndipo padzatuluka madzi amene anthu adzamwe.”+ Mose anachitadi zomwezo pamaso pa akulu a Isiraeli.