Ekisodo 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Zitatero Mose anauza Yoswa+ kuti: “Tisankhire amuna ndipo upite nawo kukamenyana ndi Aamaleki. Mawa ndikaima pamwamba pa phiri nditagwira ndodo ya Mulungu woona mʼdzanja langa.” Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:9 Nsanja ya Olonda,12/1/2002, ptsa. 9-10
9 Zitatero Mose anauza Yoswa+ kuti: “Tisankhire amuna ndipo upite nawo kukamenyana ndi Aamaleki. Mawa ndikaima pamwamba pa phiri nditagwira ndodo ya Mulungu woona mʼdzanja langa.”