-
Ekisodo 17:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Manja a Mose atatopa, anatenga mwala ndi kumuikira, ndipo anakhalapo. Aroni ndi Hura anagwira manja ake, wina dzanja lina winanso dzanja lina, moti manja ake anakhalabe okweza mpaka dzuwa kulowa.
-