Ekisodo 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nthawi yomweyo Mose anatuluka kukachingamira apongozi ake, ndipo anagwada nʼkuwerama, kenako anawakisa.* Iwo analonjerana, atatero anapita kukalowa mutenti.
7 Nthawi yomweyo Mose anatuluka kukachingamira apongozi ake, ndipo anagwada nʼkuwerama, kenako anawakisa.* Iwo analonjerana, atatero anapita kukalowa mutenti.