Ekisodo 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakakhala mlandu uliwonse atsogoleri amenewa aziweruza anthuwo. Mlandu ukakhala wovuta azibwera nawo kwa iwe,+ koma mlandu uliwonse waungʼono, aziweruza. Uwalole amunawa kuti azikuthandiza kuchita zimenezi, kuti udzichepetsere ntchito.+
22 Pakakhala mlandu uliwonse atsogoleri amenewa aziweruza anthuwo. Mlandu ukakhala wovuta azibwera nawo kwa iwe,+ koma mlandu uliwonse waungʼono, aziweruza. Uwalole amunawa kuti azikuthandiza kuchita zimenezi, kuti udzichepetsere ntchito.+