-
Ekisodo 18:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ukachita zimenezi, ndipo ngati zikugwirizana ndi zimene Mulungu akufuna, pamenepo udzaikwanitsa ntchitoyi komanso anthuwa adzabwerera kwawo akusangalala.”
-