Ekisodo 18:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kenako Mose anatsanzikana ndi apongozi ake+ ndipo iwo anabwerera kwawo.