Ekisodo 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munthu aliyense asadzakhudze wolakwayo, koma adzaponyedwe miyala kapena kulasidwa.* Kaya ndi nyama kapena munthu, adzaphedwa.’+ Koma lipenga la nyanga ya nkhosa likadzalira,+ anthu onse adzayandikire phirilo.”
13 Munthu aliyense asadzakhudze wolakwayo, koma adzaponyedwe miyala kapena kulasidwa.* Kaya ndi nyama kapena munthu, adzaphedwa.’+ Koma lipenga la nyanga ya nkhosa likadzalira,+ anthu onse adzayandikire phirilo.”