Ekisodo 19:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno Mose anatsika mʼphirimo kupita kwa anthu nʼkuyamba kuwayeretsa ndipo iwo anachapa zovala zawo.+
14 Ndiyeno Mose anatsika mʼphirimo kupita kwa anthu nʼkuyamba kuwayeretsa ndipo iwo anachapa zovala zawo.+