Ekisodo 19:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma Yehova anamuuza kuti: “Tsika, ndipo ukabwerenso limodzi ndi Aroni. Koma ansembe ndiponso anthu asadumphe malire nʼkukwera kwa Yehova kuti asawaphe.”+
24 Koma Yehova anamuuza kuti: “Tsika, ndipo ukabwerenso limodzi ndi Aroni. Koma ansembe ndiponso anthu asadumphe malire nʼkukwera kwa Yehova kuti asawaphe.”+