Ekisodo 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Musadzipangire milungu yasiliva komanso milungu yagolide kuti muziilambira pamodzi ndi ine.+