-
Ekisodo 21:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ngati anabwera ali yekha, adzachokanso ali yekha. Ngati anabwera ndi mkazi, mkazi wakeyo adzapita naye.