Ekisodo 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ngati mbuye wake wamupatsa mkazi nʼkumuberekera ana aamuna kapena aakazi, mkaziyo ndi ana ake adzakhala a mbuye wake, ndipo mwamunayo adzachoka yekha.+
4 Ngati mbuye wake wamupatsa mkazi nʼkumuberekera ana aamuna kapena aakazi, mkaziyo ndi ana ake adzakhala a mbuye wake, ndipo mwamunayo adzachoka yekha.+