Ekisodo 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma kapoloyo akanena motsimikiza kuti, ‘Ndimakonda kwambiri mbuye wanga, mkazi wanga ndi ana anga, ndipo sindikufuna kumasulidwa kuti ndichoke,’+
5 Koma kapoloyo akanena motsimikiza kuti, ‘Ndimakonda kwambiri mbuye wanga, mkazi wanga ndi ana anga, ndipo sindikufuna kumasulidwa kuti ndichoke,’+