-
Ekisodo 21:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 mbuye wakeyo azibwera naye pamaso pa Mulungu woona. Kenako azipita naye pachitseko kapena pafelemu, akatero mbuye wakeyo azimuboola khutu ndi choboolera, ndipo iye adzakhala kapolo wake moyo wake wonse.
-