Ekisodo 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngati mbuye wake sakusangalala naye ndipo sakufuna kuti akhale mkazi wake wamngʼono koma akufuna kumugulitsa kwa munthu wina,* mbuyeyo alibe ufulu womugulitsa kwa anthu a mtundu wina chifukwa wamʼchitira zachinyengo.
8 Ngati mbuye wake sakusangalala naye ndipo sakufuna kuti akhale mkazi wake wamngʼono koma akufuna kumugulitsa kwa munthu wina,* mbuyeyo alibe ufulu womugulitsa kwa anthu a mtundu wina chifukwa wamʼchitira zachinyengo.