Ekisodo 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwana wamwamunayo akakwatira mkazi wina, woyambayo asaleke kumʼpatsa chakudya, zovala komanso kugona naye monga mkazi wake.*+
10 Mwana wamwamunayo akakwatira mkazi wina, woyambayo asaleke kumʼpatsa chakudya, zovala komanso kugona naye monga mkazi wake.*+