Ekisodo 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Wina akaba munthu+ nʼkumugulitsa kapena akapezeka ndi munthu wobedwayo,+ aziphedwa.+