Ekisodo 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthu akamakangana, ndiye wina nʼkumenya mnzake ndi mwala kapena chibakera,* mnzakeyo osafa koma wavulala ndipo ali chigonere, muzichita izi:
18 Anthu akamakangana, ndiye wina nʼkumenya mnzake ndi mwala kapena chibakera,* mnzakeyo osafa koma wavulala ndipo ali chigonere, muzichita izi: