-
Ekisodo 21:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Ngati akutha kudzuka nʼkuyamba kuyendayenda kunja pogwiritsa ntchito ndodo, amene anamʼmenya uja asamalandire chilango. Koma azingopereka malipiro a nthawi imene womenyedwayo wakhala asakugwira ntchito, mpaka mnzakeyo atachiriratu.
-