Ekisodo 21:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu akamenya kapolo wake wamwamuna kapena wamkazi ndi ndodo, kapoloyo nʼkumufera, munthuyo azilangidwa ndithu.+
20 Munthu akamenya kapolo wake wamwamuna kapena wamkazi ndi ndodo, kapoloyo nʼkumufera, munthuyo azilangidwa ndithu.+