-
Ekisodo 21:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Koma ngati kapoloyo wakhalabe ndi moyo tsiku limodzi kapena masiku awiri, mbuye wakeyo sakuyenera kulangidwa chifukwa kapoloyo anamugula ndi ndalama zake.
-