-
Ekisodo 21:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Koma ngati ngʼombe inali ndi chizolowezi chogunda anthu ndipo mwiniwake anachenjezedwapo koma sankaiyangʼanira, ndiyeno yapha mwamuna kapena mkazi, ngʼombeyo iziponyedwa miyala ndipo mwiniwakeyo aziphedwanso.
-