Ekisodo 21:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ngati yagunda kapolo wamwamuna kapena wamkazi, mwiniwake azilipira ndalama zokwana masekeli* 30 kwa mbuye wa kapoloyo, ndipo ngʼombeyo iziphedwa mwa kuiponya miyala.
32 Ngati yagunda kapolo wamwamuna kapena wamkazi, mwiniwake azilipira ndalama zokwana masekeli* 30 kwa mbuye wa kapoloyo, ndipo ngʼombeyo iziphedwa mwa kuiponya miyala.