-
Ekisodo 21:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Ngati ngʼombe ya munthu yavulaza nʼkupha ngʼombe ya mnzake, azigulitsa ngʼombe yamoyoyo nʼkugawana ndalamazo komanso azigawana nyama yakufayo.
-